How to deposit

How to Deposit using Mobile Money


To deposit using BetYanga USSD application *4297#:

  1. Simply dial *4297#
  2. Select option 3. Deposit / Withdrawal
  3. On next page select option 3. Deposit using your Mobile Money (Mpamba, or Airtel Money) account.
  4. Enter the amount that you want to deposit and click SEND.
  5. You will get a POPUP from your Mobile Money account on your phone, to approve the transaction by entering your Mobile Money PIN.
  6. You will receive an SMS from your Mobile Money account, that confirms the transaction was successful. 
  7. The funds are credited on you BetYanga wallet.

Chichewa – Momwe Mungasewelere

Njira yoikira ndalama Kuzela Pa phone


Kulowetsa ndalama mu akaunti ya Betyanga pogwiritsa USSD *4297:

  1. Imbani *4297#
  2. Sankhani pa 3. ikani/chotsani
  3. Tsamba lotsatila sankhani pa 3.kuika ndalama pogwiritsa ntchito (Mpamba, Kapena Airtel Money) akaunti.
  4. Lowetsani mlingo wa ndalama zomwe mukufuna kupanga deposit kenako Tumizani.
  5. Mulandira uthenga pa phone yanu yokupemphani kuvomereza poika nambala yanu yachinsisi.
  6. Mulandira uthenga pa phone yanu yokuuzani kut zatheka. 
  7. Ndalama zanu zizaoneka ku akaunti yanu ya Betyanga.